2 Mbiri 13:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo amuna a Yuda anapfuula cokweza; ndipo popfuula amuna a Yuda, kunacitika kuti Mulungu anakantha Yerobiamu ndi Aisrayeli onse pamaso pa Abiya ndi Yuda.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:11-22