2 Mbiri 13:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ife, Yehova ndiye Mulungu wathu, sitinamsiya Iye; ndi ansembe tiri nao akutumikira Yehova ana a Aroni, ndi. Alevi, m'nchito mwao,

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:1-20