2 Mbiri 12:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Anakwera ndi magareta cikwi cimodzi mphambu mazana awiri, ndi apakavalo zikwi makumi asanu ndi limodzi, ndi anthu adadza naye kuturuka m'Aigupto ngosawerengeka, Alubi, Asuki, ndi Akusi.

2 Mbiri 12

2 Mbiri 12:2-10