2 Mbiri 12:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rehabiamu mfumu anapanga m'malo mwa izo zikopa zamkuwa, nazipereka m'manja mwa kapitao wa olindirira akusunga pakhomo pa nyumba ya mfumu.

2 Mbiri 12

2 Mbiri 12:1-16