2 Mbiri 11:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Musamuka kukayambana ndi abale anu, bwererani yense ku nyumba yace; pakuti cinthu ici cifuma kwa Ine. Ndipo anamvera mau a Yehova, nabwerera osakayambana ndi Yerobiamu.

2 Mbiri 11

2 Mbiri 11:1-7