2 Mbiri 10:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Rehabiamu mfumu anafunsana ndi akulu akulu, amene anaimirira pamaso pa Solomo atate wace akali ndi moyo, nati, Mundipangire bwanji, kuti ndiwabwezere mau anthu awa?

2 Mbiri 10

2 Mbiri 10:2-9