2 Mbiri 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, atamva Yerobiamu mwana wa Nebati (popeza anali m'Aigupto kumene adathawira, kuthawa Solomo mfumu), Yerobiamu anabwera kucoka ku Aigupto.

2 Mbiri 10

2 Mbiri 10:1-3