2 Mbiri 10:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo mfumu siinamvera anthuwo; pakuti kusinthaku kudafuma kwa Mulungu, kuti Yehova akhazikitse mau ace, amene ananenetsa Ahiya wa ku Silo kwa Yerobiamu mwana wa Nebati.

2 Mbiri 10

2 Mbiri 10:6-19