2 Mbiri 10:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, popeza atate wanga anakusenzetsani goli lolemera, ine ndidzaonjezerapo pa goli lanu; atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.

2 Mbiri 10

2 Mbiri 10:1-14