2 Mbiri 1:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsopano, Yehova Mulungu, likhazikike lonjezano lanu la kwa Davide atate wanga; pakuti mwandiika mfumu ya anthu akucuruka ngati pfumbi lapansi.

2 Mbiri 1

2 Mbiri 1:1-11