2 Mafumu 9:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanyamuka, nalowa m'nyumba; ndipo anatsanulira mafutawo pamutu pace, nanena naye, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Ndakudzoza ukhale mfumu ya pa anthu a Yehova, ndiwo Aisrayeli.

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:5-10