2 Mafumu 9:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma anakweza maso ace kuzenera, nati, Ali ndi ine ndani? Ndani? Nampenyererako adindo awiri kapena atatu.

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:28-34