2 Mafumu 9:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anamuka wapakavalo kukomana naye, nati, Atero mfumu, Mtendere kodi? Nati Yehu, Ngwanji mtendere, tembenukira m'mbuyo mwanga. Ndi mlonda anawafotokozera kuti, Mthenga wawafika, koma wosabwera.

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:11-24