2 Mafumu 9:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nayenda Yehu m'gareta, namuka ku Yezreeli, popeza Yoramu anagonako; ndi Ahaziya mfumu ya Yuda anatsikira kukamuona Yoramu.

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:15-23