2 Mafumu 9:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero Yehu mwana wa Yehosafati mwana wa Nimsi anapandukira Yoramu. Tsono Yoramu atalindira ku Ramoti Gileadi, iye ndi Aisrayeli onse, cifukwa ca Hazaeli mfumu ya Aramu;

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:6-24