2 Mafumu 9:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo agaru adzamudya Yezebeli pa dera la Yezreeli, wopanda wina wakumuika. Pamenepo anatsegula pakhomo, nathawa.

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:7-11