2 Mafumu 8:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofunsa mfumu, mkaziyo anaisimbira. Pamenepo mfumu anamuikira mdindo, ndi kuti, Bwezetsa zace zonse ndi zipatso zonse za m'munda, cicokere iye m'dziko mpaka lero lino.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:1-9