2 Mafumu 8:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakutha pace pa zaka zisanu ndi ziwirizo, mkaziyo anabwera kucoka m'dziko la Afilisti, naturuka kukanena za nyumba yace ndi munda wace kwa mfumu.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:1-8