2 Mafumu 8:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nagona Yoramu ndi makolo ace, naikidwa pamodzi ndi makolo ace m'mudzi wa Davide; ndipo Ahaziya mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:14-29