2 Mafumu 8:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yoramu anaoloka kumka ku Zairi, ndi magareta ace onse pamodzi naye; nauka iye usiku, nakantha Aedomu akumzinga ndi nduna za magareta, nathawira anthu ku mahema ao.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:13-29