2 Mafumu 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Hazaeli, Koma nanga kapolo wanu ali ciani, ndiye garu, kuti akacite cinthu cacikuru ici? Nayankha Elisa, Yehova wandionetsa kuti udzakhala mfumu ya pa Aramu.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:8-18