2 Mafumu 8:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa ananena ndi mkazi uja adamuukitsira mwana wace, kuti, Nyamuka, numuke iwe ndi banja lako, nugonere komwe ukaone malo; pakuti Yehova waitana njala, nidzagwera dziko zaka zisanu ndi ziwiri.

2 Mafumu 8

2 Mafumu 8:1-11