2 Mafumu 7:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunacitika, monga adanena munthu wa Mulungu kwa mfumu, ndi kuti, Adzagula miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, adzagulanso muyeso wa ufa ndi sekeli; kudzatero mawa, dzuwa lino, pa cipata ca Samariya;

2 Mafumu 7

2 Mafumu 7:17-20