2 Mafumu 5:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Elisa anamtumira mthenga, ndi kuti, Kasambe m'Yordano kasanu ndi kawiri, ndi mnofu wako udzabwerera momwe, nudzakhala wokonzeka.

2 Mafumu 5

2 Mafumu 5:1-14