2 Mafumu 4:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nawatsogolera Gehazi, naika ndodo pankhope pa mwanayo; koma mwanayo analibe mau, kapena kusamalira. Motero anabwerera kukomana naye, namuuza kuti, Sanauke mwanayo.

2 Mafumu 4

2 Mafumu 4:25-36