2 Mafumu 25:29-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

29. Nasintha zobvala zace za m'kaidi, namadya iye mkate pamaso pace masiku onse a moyo wace.

30. Ndi kunena za cakudya cace, panali cakudya cosalekeza copatsidwa kwa iye ndi mfumu, tsiku Uri lonse gawo lace, masiku onse a moyo wace.

2 Mafumu 25