2 Mafumu 25:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nawalumbirira Gedaliya iwo ndi anthu ao, nanena nao, Musamaopa anyamata a Akasidi; khalani m'dziko; tumikirani mfumu ya Babulo, ndipo kudzakukomerani.

2 Mafumu 25

2 Mafumu 25:14-28