2 Mafumu 25:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kunena za anthu otsalira m'dziko la Yuda, amene adawasiya Nebukadinezara mfumu ya Babulo, iyeyu anamuika Gedaliya mwana wa Ahikamu mwana wa Safani akhale wowalamulira.

2 Mafumu 25

2 Mafumu 25:17-30