2 Mafumu 25:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zoimiritsa zamkuwa zinali m'nyumba ya Yehova, ndi maphaka ace, ndi thawale lamkuwa, zinali m'nyumba ya Yehova, Akasidi anazithyolathyola, natenga mkuwa wace kumka nao ku Babulo.

2 Mafumu 25

2 Mafumu 25:7-21