2 Mafumu 24:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mfumu ya Aigupto sinabwerezanso kuturuka m'dziko lace, pakuti mfumu ya Babulo idalanda kuyambira ku mtsinje wa Aigupto kufikira ku mtsinje Firate, ndilo lonse anali nalo mfumu ya Aigupto.

2 Mafumu 24

2 Mafumu 24:1-14