2 Mafumu 24:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Zedekiya anali wa zaka makumi awiri mphambu cimodzi polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka khumi ndi cimodzi m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Hamutala mwana wa Yeremiya wa ku Libina.

2 Mafumu 24

2 Mafumu 24:16-20