2 Mafumu 24:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturutsa kucotsa komweko cuma conse ca nyumba ya Yehova, ndi cuma ca nyumba ya mfumu, naduladula zipangizo zonse zagolidi adazipanga Solomo mfumu ya Israyeli m'Kacisi wa Yehova, monga Yehova adanena.

2 Mafumu 24

2 Mafumu 24:10-19