2 Mafumu 23:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yoyakimu anali wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka khumi ndi cimodzi m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Zebida mwana wa Pedaya wa Ruma.

2 Mafumu 23

2 Mafumu 23:26-37