2 Mafumu 23:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yoahazi anali wa zaka makumi awiri mphambu zitatu polowa ufumu wace, nakhala mfumu miyezi itatu m'Yerusalemu ndi dzina la mace ndiye Hamutali mwana wa Yeremiya wa ku Libina.

2 Mafumu 23

2 Mafumu 23:28-37