2 Mafumu 23:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yehova sanakululuka mkwiyo wace waukuru waukali umene adapsa mtima nao pa Yuda, cifukwa ca zoputa zonse Manase adaputa nazo mkwiyo wace.

2 Mafumu 23

2 Mafumu 23:17-28