2 Mafumu 22:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

popeza mtima wako ngoolowa, ndipo unadzicepetsa pamaso pa Yehova muja udamva zonenera Ine malo ana ndi anthu okhalamo, kuti adzakhala abwinja, ndi temberero; ndipo unang'amba zobvala zako ndi kulira misozi pamaso panga, Inenso ndakumvera, ati Yehova.

2 Mafumu 22

2 Mafumu 22:16-20