2 Mafumu 21:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Napititsa mwana wace pamoto, naombeza maula, nacita zanyanga, naika obwebweta ndi openda; anacita zoipa zambiri pamaso pa Yehova kuutsa mkwiyo wace.

2 Mafumu 21

2 Mafumu 21:1-11