2 Mafumu 21:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amoni anali wa zaka makumi awiri mphambu ziwiri polowa iye ufumu wace, nakhala mfumu zaka ziwiri m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Mesulemeti mwana wa Haruzi wa ku Yotiba.

2 Mafumu 21

2 Mafumu 21:17-26