2 Mafumu 21:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzataya cotsala ca colowa canga, ndi kuwapereka m'dzanja la adani ao, nadzakhala iwo cakudya ndi cofunkha ca adani ao onse;

2 Mafumu 21

2 Mafumu 21:6-19