2 Mafumu 21:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Manase anali wa zaka khumi ndi ziwiri polowa iye ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi asanu ndi zisanu m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Hefisiba.

2 Mafumu 21

2 Mafumu 21:1-6