2 Mafumu 20:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Yesaya mneneri anadza kwa mfumu Hezekiya, nati kwa iye, Anatani anthu awa? anadza kwa inu kufumira kuti? Nati Hezekiya, Afumira dziko la kutari ku Babulo.

2 Mafumu 20

2 Mafumu 20:8-15