2 Mafumu 2:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliya anagwira copfunda cace, nacipindapinda napanda madzi, nagawikana kwina ndi kwina; ndipo anaoloka iwo onse awiri pansi pouma.

2 Mafumu 2

2 Mafumu 2:2-13