2 Mafumu 2:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ana a aneneri okhala ku Yeriko anayandikira kwa Elisa, nanena naye, Kodi udziwa kuti Yehova akucotsera lero mbuye wako, mtsogoleri wako? Nati iye, Inde ndidziwa, khalani muli cete.

2 Mafumu 2

2 Mafumu 2:1-10