2 Mafumu 2:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ana a aneneri okhala ku Beteli anaturukira Elisa, nanena naye, Kodi udziwa kuti Yehova akucotsera lero mbuye wako, mtsogoleri wako? Nati, lode ndidziwa, khalani muli cete.

2 Mafumu 2

2 Mafumu 2:1-12