2 Mafumu 2:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anatenga copfunda ca Eliya cidamtayikiraco, napanda madziwo, nati, Ali kuti Yehova Mulungu wa Eliya? Ndipo atapanda madziwo anagawikana kwina ndi kwina, naoloka Elisa.

2 Mafumu 2

2 Mafumu 2:13-23