2 Mafumu 19:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati kwa iye, Atero Hezekiya, Lero line ndilo tsiku la cisautso, ndi la kudzudzula, ndi la kunyoza; pakuti ana anafikira kubadwa, koma palibe mphamvu yakubala.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:1-13