2 Mafumu 19:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ici ndi cizindikilo cako: caka cino mudzadya za mphulumukwa, ndi caka ca mawa za mankhokwe, ndi caka camkuca muzibzala ndi kukolola, muzioka minda yampesa ndi kudya zipatso zace.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:22-30