2 Mafumu 19:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sunamva kodi kuti Ine ndinacicita kale lomwe, ndi kucipanga masiku akalekale? tsopano ndacifikitsa kuli iwe, uzikhala wakupasula imidzi yamalinga ikhale miunda ya mabwinja.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:24-35