2 Mafumu 19:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiye yani wamtonza ndi kumcitira mwano? ndiye yani wamkwezera mau ndi kumgadamira maso ako m'mwamba? Ndiye Woyerayo wa Israyeli.

2 Mafumu 19

2 Mafumu 19:15-23