2 Mafumu 18:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kazembeyo ananena nao, Ngati mbuyanga ananditumiza kwa mbuyako, ndi kwa iwe, kunena mau awa? si kwa anthu awa nanga okhala palinga, kuti akadye zonyansa zao, ndi kumwa mkodzo wao pamodzi ndi inu?

2 Mafumu 18

2 Mafumu 18:17-37